Maliko 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma Yesu anawaitana, ndipo atafika kwa iye, anawauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati akulamulira anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+ Luka 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, panabuka mkangano woopsa pakati pawo za amene anali kuoneka wamkulu kwambiri.+
42 Koma Yesu anawaitana, ndipo atafika kwa iye, anawauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati akulamulira anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+