Miyambo 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 pakuti ukumuunjikira makala amoto pamutu pake,+ ndipo Yehova adzakupatsa mphoto.+