Levitiko 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova. Mateyu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,+ komanso lakuti, Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+ Mateyu 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Lachiwiri lofanana nalo ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Luka 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndani mwa atatuwa amene iweyo ukuona kuti anakonda+ munthu amene anakumana ndi achifwambayu?”
18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.