Yesaya 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Yehova wanena kuti: “Anthu inu, tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama.+ Pakuti chipulumutso changa chatsala pang’ono kubwera,+ ndipo chilungamo changa chatsala pang’ono kuonekera.+
56 Yehova wanena kuti: “Anthu inu, tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama.+ Pakuti chipulumutso changa chatsala pang’ono kubwera,+ ndipo chilungamo changa chatsala pang’ono kuonekera.+