Mateyu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Lekani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, Yakobo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu wopereka lamulo ndi woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani, kuti uziweruza mnzako?+
12 Komatu wopereka lamulo ndi woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani, kuti uziweruza mnzako?+