Yeremiya 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sipadzasowa munthu wa m’banja la Yonadabu mwana wa Rekabu woima+ pamaso panga kuti azinditumikira nthawi zonse.”’”+
19 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sipadzasowa munthu wa m’banja la Yonadabu mwana wa Rekabu woima+ pamaso panga kuti azinditumikira nthawi zonse.”’”+