1 Akorinto 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense asamangodzifunira zopindulitsa iye yekha basi,+ koma zopindulitsanso wina.+