1 Akorinto 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano ndikukulimbikitsani mokudandaulirani, abale, kuti: Mukudziwa kuti banja la Sitefana ndilo chipatso choyambirira+ mu Akaya ndi kuti anadzipereka kutumikira oyera.+
15 Tsopano ndikukulimbikitsani mokudandaulirani, abale, kuti: Mukudziwa kuti banja la Sitefana ndilo chipatso choyambirira+ mu Akaya ndi kuti anadzipereka kutumikira oyera.+