1 Akorinto 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale onse akukupatsani moni. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.+ 2 Akorinto 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwaubale.+ 1 Atesalonika 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Perekani moni kwa abale onse ndi kupsompsonana kwaubale.+ 1 Petulo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+
14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+