Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Atesalonika 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano tikukulangizani+ abale m’dzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti mupewe+ m’bale aliyense woyenda mosalongosoka+ komanso mosagwirizana ndi mwambo umene tinakupatsani.+

  • 2 Atesalonika 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati wina sakumvera mawu athu+ a m’kalatayi, muikeni chizindikiro+ ndipo lekani kuchitira naye zinthu limodzi,+ kuti achite manyazi.+

  • Tito 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu wolimbikitsa mpatuko,+ usagwirizane+ nayenso utamudzudzula koyamba ndi kachiwiri,+

  • 2 Yohane 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena