Akolose 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikunena zimenezi kuti munthu aliyense asakunyengeni ndi mfundo zokopa.+ Tito 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa.
10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa.