Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Aefeso 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera+ padzasonyezedwe chuma chopambana+ cha kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anatisonyeza mogwirizana+ ndi Khristu Yesu.
7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+
7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera+ padzasonyezedwe chuma chopambana+ cha kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anatisonyeza mogwirizana+ ndi Khristu Yesu.