2 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake. Aefeso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndiponso kuti mudziwe chikondi cha Khristu+ chimene chimaposa kudziwa zinthu zonse, kuti mudzazidwe ndi makhalidwe onse+ amene Mulungu amapereka.
9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake.
19 ndiponso kuti mudziwe chikondi cha Khristu+ chimene chimaposa kudziwa zinthu zonse, kuti mudzazidwe ndi makhalidwe onse+ amene Mulungu amapereka.