Luka 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kuti zimene anthu ambiri akuganiza mumtima mwawo zionekere poyera.+ Koma iwe lupanga lalitali lidzalasa moyo wako.”+ 1 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.
35 kuti zimene anthu ambiri akuganiza mumtima mwawo zionekere poyera.+ Koma iwe lupanga lalitali lidzalasa moyo wako.”+
4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.