Machitidwe 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zitatero, onse anagwira Sositene,+ mtsogoleri wa sunagoge ndi kuyamba kumumenya pafupi ndi mpando woweruzira milanduwo. Koma Galiyo sanasamale zimenezo ngakhale pang’ono.
17 Zitatero, onse anagwira Sositene,+ mtsogoleri wa sunagoge ndi kuyamba kumumenya pafupi ndi mpando woweruzira milanduwo. Koma Galiyo sanasamale zimenezo ngakhale pang’ono.