1 Akorinto 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano kunena za amene sali pabanja,* ndilibe lamulo lililonse la Ambuye, koma ndikupereka maganizo anga+ monga munthu amene ndinasonyezedwa chifundo ndi Ambuye+ kuti ndikhale wokhulupirika.+ 2 Akorinto 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni.
25 Tsopano kunena za amene sali pabanja,* ndilibe lamulo lililonse la Ambuye, koma ndikupereka maganizo anga+ monga munthu amene ndinasonyezedwa chifundo ndi Ambuye+ kuti ndikhale wokhulupirika.+
8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni.