Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+ Aroma 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ngati m’bale wako akuvutika maganizo chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukuyendanso m’chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera+ chifukwa cha zakudya zanu.
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
15 Chifukwa ngati m’bale wako akuvutika maganizo chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukuyendanso m’chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera+ chifukwa cha zakudya zanu.