1 Akorinto 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 M’malomwake, pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zazikulu.+ Komabe, ine ndikuonetsani njira yopambana.+
31 M’malomwake, pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zazikulu.+ Komabe, ine ndikuonetsani njira yopambana.+