Machitidwe 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anali okwiya chifukwa atumwiwo anali kuphunzitsa anthu ndi kulalikira mosapita m’mbali za kuuka kwa akufa pogwiritsa ntchito chitsanzo cha Yesu.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
2 Iwo anali okwiya chifukwa atumwiwo anali kuphunzitsa anthu ndi kulalikira mosapita m’mbali za kuuka kwa akufa pogwiritsa ntchito chitsanzo cha Yesu.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”