Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ndiponso pogwiritsa ntchito mphamvu yochita zizindikiro ndi zinthu zodabwitsa zolosera zam’tsogolo,+ mwa mphamvu ya mzimu woyera. Chotero ndalalikira mokwanira uthenga wabwino wonena za Khristu+ kuyambira ku Yerusalemu, kuzungulira+ mpaka ku Iluriko.

  • 1 Akorinto 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pakuti ufumu wa Mulungu sunagone m’mawu, koma mu mphamvu.+

  • 1 Atesalonika 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chifukwa pamene tinali kulalikira uthenga wabwino kwa inu, sitinali kungolankhula basi, koma uthengawo unakukhudzani kwambiri, komanso unabwera limodzi ndi mphamvu+ ya mzimu woyera, ndipo unachititsa kuti mukhale otsimikiza+ mtima kwambiri. Ndipo inuyo mukudziwa zimene tinakuchitirani pofuna kukuthandizani.+

  • 2 Petulo 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndithudi, pamene ifeyo tinakudziwitsani za mphamvu ya Ambuye wathu Yesu Khristu ndi za kukhalapo* kwake,+ sitinatengere nkhani zabodza zopekedwa mochenjera ndi anthu,+ koma tinachita zimenezo chifukwa tinachita kuona ndi maso athu ulemerero wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena