1 Akorinto 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhani yokhudza mtengo wozunzikirapowo ndi chinthu chopusa+ kwa anthu amene akupita kukawonongedwa,+ koma kwa ife amene tikupulumutsidwa+ ndi mphamvu ya Mulungu.+ 2 Akorinto 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+
18 Nkhani yokhudza mtengo wozunzikirapowo ndi chinthu chopusa+ kwa anthu amene akupita kukawonongedwa,+ koma kwa ife amene tikupulumutsidwa+ ndi mphamvu ya Mulungu.+
14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+