Machitidwe 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino. Machitidwe 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mulungu wa makolo athu anaukitsa+ Yesu, amene inu munamupha mwa kumupachika pamtengo.+
10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.