Numeri 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova akuyang’aneni mokondwera+ ndipo akupatseni mtendere.”’+ Afilipi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.
7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.