Akolose 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pogwiritsa ntchito mtengo wozunzikirapowo, iye anavula maboma ndi olamulira n’kuwasiya osavala,+ ndipo anawaonetsa poyera pamaso pa anthu onse kuti aliyense aone kuti wawagonjetsa,+ n’kumayenda nawo ngati akaidi.+
15 Pogwiritsa ntchito mtengo wozunzikirapowo, iye anavula maboma ndi olamulira n’kuwasiya osavala,+ ndipo anawaonetsa poyera pamaso pa anthu onse kuti aliyense aone kuti wawagonjetsa,+ n’kumayenda nawo ngati akaidi.+