Afilipi 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndapanikizika ndi zinthu ziwirizi,+ koma chimene ndikufuna ndicho kumasuka ndi kukhala ndi Khristu.+ Pakuti kunena zoona, chimenechi ndiye chabwino kwambiri.+
23 Ndapanikizika ndi zinthu ziwirizi,+ koma chimene ndikufuna ndicho kumasuka ndi kukhala ndi Khristu.+ Pakuti kunena zoona, chimenechi ndiye chabwino kwambiri.+