Aheberi 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kulandira chilango chochokera kwa Mulungu wamoyo n’chinthu choopsa.+ 1 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso, ngati mukupempha zinthu kwa Atate, amene amaweruza mopanda tsankho+ malinga ndi ntchito za aliyense, chitani zinthu ndi mantha+ pa nthawi imene muli ngati alendo m’dzikoli.+
17 Ndiponso, ngati mukupempha zinthu kwa Atate, amene amaweruza mopanda tsankho+ malinga ndi ntchito za aliyense, chitani zinthu ndi mantha+ pa nthawi imene muli ngati alendo m’dzikoli.+