12 Pakuti sitidzayesa n’komwe kudziona ngati ndife ofanana ndi anthu enaake kapena kudziyerekezera ndi ena amene amadzikweza.+ Ndithudi anthu amenewo samvetsa kanthu kalikonse chifukwa akuyezana okhaokha pogwiritsira ntchito miyezo yawo yomwe, ndipo akudziyerekezera ndi iwo eni.+