Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ 2 Timoteyo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.
18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.