Afilipi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+ 1 Atesalonika 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?
16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+
19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?