Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. Afilipi 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti ndilibe wina wamtima ngati iye, amene angasamaledi+ za inu moona mtima.
16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.