Aroma 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abale amene ali ku Makedoniya ndi ku Akaya+ akhala ali ofunitsitsa kupereka+ mphatso kwa oyera osauka a ku Yerusalemu. 1 Akorinto 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+ 2 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+ 2 Akorinto 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zili choncho chifukwa utumiki wothandiza anthu umenewu si kuti ukungopatsa oyerawo zinthu zochuluka zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso anthu ambiri kupereka mapemphero ochuluka oyamika Mulungu.
26 Abale amene ali ku Makedoniya ndi ku Akaya+ akhala ali ofunitsitsa kupereka+ mphatso kwa oyera osauka a ku Yerusalemu.
16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+
4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+
12 Zili choncho chifukwa utumiki wothandiza anthu umenewu si kuti ukungopatsa oyerawo zinthu zochuluka zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso anthu ambiri kupereka mapemphero ochuluka oyamika Mulungu.