2 Akorinto 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zimenezi zinatichititsa kuti timulimbikitse Tito+ kuti, popeza iye ndiye anayambitsa zoperekazi pakati panu, iyeyo amalizitse kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo.
6 Zimenezi zinatichititsa kuti timulimbikitse Tito+ kuti, popeza iye ndiye anayambitsa zoperekazi pakati panu, iyeyo amalizitse kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo.