1 Akorinto 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+ 1 Akorinto 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+
10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+
15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+