Aroma 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti sindidzayesa m’pang’ono pomwe kulankhula kanthu ngakhale kamodzi kokha ngati sikanachokere m’zinthu zimene Khristu anachita mwa ine+ kuti mitundu ina ikhale yomvera.+ Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu anga+ ndi zochita zanga, 1 Akorinto 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndaweruza kuti m’dzina la Ambuye wathu Yesu, mukakumana pamodzi, komanso ndi mzimu wanga ndi mphamvu ya Ambuye wathu Yesu,+
18 Pakuti sindidzayesa m’pang’ono pomwe kulankhula kanthu ngakhale kamodzi kokha ngati sikanachokere m’zinthu zimene Khristu anachita mwa ine+ kuti mitundu ina ikhale yomvera.+ Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu anga+ ndi zochita zanga,
4 Ndaweruza kuti m’dzina la Ambuye wathu Yesu, mukakumana pamodzi, komanso ndi mzimu wanga ndi mphamvu ya Ambuye wathu Yesu,+