1 Akorinto 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+ 1 Yohane 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene taziona ndi kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe.+ Ndipotu, ifeyo ndife ogwirizana+ ndi Atate ndi Mwana wake Yesu Khristu.+
9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+
3 Zimene taziona ndi kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe.+ Ndipotu, ifeyo ndife ogwirizana+ ndi Atate ndi Mwana wake Yesu Khristu.+