Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ukalankhule naye ndi kumuuza zokanena.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye pamene mukulankhula,*+ ndipo ndidzakuuzani zochita.+

  • Afilipi 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti Mulungu amachita zinthu m’njira imene imamusangalatsa. Iye amalimbitsa zolakalaka zanu+ kuti muchite zinthu zonse zimene iye amakonda.+

  • 1 Yohane 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Inuyo, Mulungu anakudzozani ndi mzimu+ ndipo mzimu umenewo udakali mwa inu. Chotero simukufunikira wina aliyense kuti azikuphunzitsani,+ koma popeza kuti munadzozedwadi moona+ osati monama, chifukwa cha kudzozedwako, mukuphunzitsidwa zinthu zonse.+ Monga mmene mwaphunzitsidwira, pitirizani kukhala ogwirizana+ naye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena