Aefeso 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi,+ omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu.+ Kudzeranso mwa iye, mutakhulupirira munaikidwa chidindo+ cha mzimu woyera wolonjezedwawo,+ Aheberi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+
13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi,+ omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu.+ Kudzeranso mwa iye, mutakhulupirira munaikidwa chidindo+ cha mzimu woyera wolonjezedwawo,+
4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+