Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.” 1 Petulo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+
4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”
6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+