Machitidwe 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+ Aroma 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, popeza tsopano tayesedwa olungama chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro,+ tiyeni tikhale pa mtendere+ ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu. Aroma 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndani adzasumira mlandu anthu a Mulungu ochita kusankhidwa?+ Mulungu ndiye amawayesa olungama.+
39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+
5 Chotero, popeza tsopano tayesedwa olungama chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro,+ tiyeni tikhale pa mtendere+ ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.