Genesis 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova,+ Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala pakati pawo.+
3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova,+ Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala pakati pawo.+