Genesis 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndidzamudalitsa ndipo iwe ndidzakupatsa mwana wamwamuna wochokera mwa iye.+ Ndidzamudalitsa ndipo adzakhala mayi wa mitundu yambiri ya anthu+ ndi wa mafumu a mitundu yambiri ya anthu.”+
16 Iye ndidzamudalitsa ndipo iwe ndidzakupatsa mwana wamwamuna wochokera mwa iye.+ Ndidzamudalitsa ndipo adzakhala mayi wa mitundu yambiri ya anthu+ ndi wa mafumu a mitundu yambiri ya anthu.”+