Afilipi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+
18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+