Machitidwe 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, ndipo anamuuza kuti: “M’bale, kodi ukuona kuchuluka kwa okhulupirira amene ali pakati pa Ayuda? Ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+
20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, ndipo anamuuza kuti: “M’bale, kodi ukuona kuchuluka kwa okhulupirira amene ali pakati pa Ayuda? Ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+