Akolose 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalanibe ozikika mozama+ mwa iye, ndipo monga mmene munaphunzitsidwira, pitirizani kukula+ pamene mukumuona iye monga maziko anu, ndi kukhazikika m’chikhulupiriro.+ Sefukiranibe ndi chikhulupiriro popereka mapemphero oyamikira.+
7 Khalanibe ozikika mozama+ mwa iye, ndipo monga mmene munaphunzitsidwira, pitirizani kukula+ pamene mukumuona iye monga maziko anu, ndi kukhazikika m’chikhulupiriro.+ Sefukiranibe ndi chikhulupiriro popereka mapemphero oyamikira.+