Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Akolose 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Musalole kuti munthu aliyense amene amasangalala ndi kudzichepetsa kwachinyengo komanso ndi kulambira angelo akumanitseni+ mphotoyo.+ Anthu oterowo amaumirira zinthu zimene aona ndipo maganizo awo ochimwa amawachititsa kudzitukumula popanda chifukwa chomveka.

  • Aheberi 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Musatengeke ndi ziphunzitso zosiyanasiyana zachilendo.+ Ndi bwino kuti mtima ukhale wolimba chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu,+ osati chifukwa cha zakudya.+ Pakuti amene amatanganidwa ndi zakudyazo sakupindula nazo.

  • 1 Petulo 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena