1 Atesalonika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani. 2 Atesalonika 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+
11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.
10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+