Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+
12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+