1 Akorinto 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu.
22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu.