Afilipi 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akatero ndiye kuti achita chiyani? Palibe! Mulimonse mmene zingakhalire, kaya ndi mwachiphamaso+ kapena m’choonadi, Khristu akufalitsidwabe.+ Choncho ine ndikukondwera. Ndipotu ndipitiriza kukondwera,
18 Akatero ndiye kuti achita chiyani? Palibe! Mulimonse mmene zingakhalire, kaya ndi mwachiphamaso+ kapena m’choonadi, Khristu akufalitsidwabe.+ Choncho ine ndikukondwera. Ndipotu ndipitiriza kukondwera,