Mateyu 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Lekani kudera nkhawa+ moyo wanu kuti mudzadya chiyani, kapena mudzamwa chiyani, kapenanso kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo suposa chakudya, ndipo kodi thupi siliposa chovala?+ Luka 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Pa chifukwa chimenechi ndikukuuzani kuti, Lekani kudera nkhawa moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa matupi anu kuti mudzavala chiyani.+ 1 Petulo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chitani zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ pakuti amakuderani nkhawa.+
25 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Lekani kudera nkhawa+ moyo wanu kuti mudzadya chiyani, kapena mudzamwa chiyani, kapenanso kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo suposa chakudya, ndipo kodi thupi siliposa chovala?+
22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Pa chifukwa chimenechi ndikukuuzani kuti, Lekani kudera nkhawa moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa matupi anu kuti mudzavala chiyani.+